Numeri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene Aisiraeliwo anali pa ulendo kuchokera kuphiri la Hora+ kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira, kulambalala dziko la Edomu,+ anayamba kutopa chifukwa cha njirayo. Numeri 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Malire anu a kumpoto akayende motere: Mukalembe malirewo kuchokera ku Nyanja Yaikulu mpaka kuphiri la Hora.+
4 Pamene Aisiraeliwo anali pa ulendo kuchokera kuphiri la Hora+ kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira, kulambalala dziko la Edomu,+ anayamba kutopa chifukwa cha njirayo.
7 “‘Malire anu a kumpoto akayende motere: Mukalembe malirewo kuchokera ku Nyanja Yaikulu mpaka kuphiri la Hora.+