Numeri 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Tsopano awa ndi mayina a amuna owerengedwa mwa Alevi+ malinga ndi mabanja awo: Agerisoni, a banja la Gerisoni,+ Akohati, a banja la Kohati,+ ndi Amerari, a banja la Merari.+ 1 Mbiri 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anawagawa m’magulu+ ndi kuwapereka kwa ana a Levi.+ Anawapereka kwa Gerisoni, Kohati, ndi Merari.
57 Tsopano awa ndi mayina a amuna owerengedwa mwa Alevi+ malinga ndi mabanja awo: Agerisoni, a banja la Gerisoni,+ Akohati, a banja la Kohati,+ ndi Amerari, a banja la Merari.+
6 Ndiyeno Davide anawagawa m’magulu+ ndi kuwapereka kwa ana a Levi.+ Anawapereka kwa Gerisoni, Kohati, ndi Merari.