Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+

  • Nehemiya 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo.

  • Salimo 78:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iye anapitiriza kuwatsogolera ndi mtambo masana,+

      Ndipo usiku wonse anali kuwatsogolera ndi kuwala kwa moto.+

  • Salimo 105:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Mulungu anayala mtambo kuti uziwatchinga,+

      Ndipo anawapatsa moto kuti uziwaunikira usiku.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena