Numeri 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma akazi achimidiyani ndi ana awo anawagwira ndi kuwatenga kupita nawo kwawo.+ Anafunkhanso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse. Deuteronomo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma musaphe akazi, ana aang’ono,+ ziweto+ ndi chilichonse chopezeka mumzindawo. Muzifunkha+ zinthu zonse za mumzindawo ndipo muzidya zimene mwafunkha kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
9 Koma akazi achimidiyani ndi ana awo anawagwira ndi kuwatenga kupita nawo kwawo.+ Anafunkhanso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse.
14 Koma musaphe akazi, ana aang’ono,+ ziweto+ ndi chilichonse chopezeka mumzindawo. Muzifunkha+ zinthu zonse za mumzindawo ndipo muzidya zimene mwafunkha kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+