Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+ Salimo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+ Miyambo 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Umakhala msampha munthu wochokera kufumbi akathamangira kufuula kuti, “N’zoyera!”+ koma pambuyo polonjeza+ n’kumafuna kuganiziranso bwino.+
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+
25 Umakhala msampha munthu wochokera kufumbi akathamangira kufuula kuti, “N’zoyera!”+ koma pambuyo polonjeza+ n’kumafuna kuganiziranso bwino.+