Mlaliki 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+ Malaki 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.” Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?” “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka. Maliko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu inu mumanena kuti, ‘Munthu akauza bambo ake kapena mayi ake kuti: “Chilichonse chimene ine ndili nacho, chimene mukanatha kupindula nacho, ndi khobani,+ (kutanthauza kuti, mphatso yoperekedwa+ kwa Mulungu,)”’ . . .
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+
8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.” Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?” “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.
11 Koma anthu inu mumanena kuti, ‘Munthu akauza bambo ake kapena mayi ake kuti: “Chilichonse chimene ine ndili nacho, chimene mukanatha kupindula nacho, ndi khobani,+ (kutanthauza kuti, mphatso yoperekedwa+ kwa Mulungu,)”’ . . .