Deuteronomo 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero muzisunga mosamala malangizo onse ndi zigamulo zonse+ zimene ndikuika pamaso panu lero.+ Deuteronomo 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Lero Yehova Mulungu wanu akukulamulani kutsatira malangizo ndi zigamulo+ zimenezi. Motero muzisunga ndi kutsatira zimenezi ndi mtima wanu+ wonse ndi moyo wanu wonse.+ Luka 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma iye anati: “Ayi, m’malomwake, Odala ndi amene akumva mawu a Mulungu ndi kuwasunga!”+
16 “Lero Yehova Mulungu wanu akukulamulani kutsatira malangizo ndi zigamulo+ zimenezi. Motero muzisunga ndi kutsatira zimenezi ndi mtima wanu+ wonse ndi moyo wanu wonse.+