Deuteronomo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati panu, kuchokera pakati pa abale anu, ndipo inu mudzamvere mneneri ameneyo.+ Machitidwe 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+ Machitidwe 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Ameneyu ndi Mose amene anauza ana a Isiraeli kuti, ‘Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati pa abale anu.’+
15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati panu, kuchokera pakati pa abale anu, ndipo inu mudzamvere mneneri ameneyo.+
22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+
37 “Ameneyu ndi Mose amene anauza ana a Isiraeli kuti, ‘Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati pa abale anu.’+