4 Iwo anakaonekera pamaso pa wansembe Eleazara,+ Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri, ndi kuwauza kuti: “Yehova ndiye analamula Mose kuti atipatse cholowa pakati pa abale athu.”+ Choncho anawapatsa cholowa pakati pa abale a bambo awo, pomvera lamulo la Yehova.+