Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+

  • Yoswa 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Palibe tsiku lina lofanana ndi limenelo, kaya pambuyo pake kapena patsogolo pake, loti Yehova anamvera mawu a munthu mwa njira imeneyi,+ popeza Yehova mwiniyo anali kumenyera nkhondo Isiraeli.+

  • Yoswa 10:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Yoswa anagwira mafumu onsewa n’kulanda malo awo pa nthawi imodzi,+ chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndiye anali kuwamenyera nkhondo.+

  • Salimo 44:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+

      Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+

      Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,

      Chifukwa munakondwera nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena