Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova adzakumenyerani nkhondo,+ ndipo inu mudzakhala chete, osachitapo kalikonse.”

  • Deuteronomo 1:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+

  • Deuteronomo 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amuna inu, musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo.’+

  • Yoswa 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Inuyo mwaona zonse zimene Yehova Mulungu wanu anachitira mitundu yonse chifukwa cha inu.+ Yehova Mulungu wanu ndiye anali kukumenyerani nkhondo.+

  • Salimo 33:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Moyo wathu wakhala ukuyembekeza Yehova.+

      Iye ndi mthandizi wathu ndi chishango chathu.+

  • Yesaya 42:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+

  • Zekariya 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Yehova adzapita kukamenyana ndi anthu a mitundu inawo+ ngati mmene anachitira pomenyana ndi adani ake m’mbuyomu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena