Numeri 33:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 “‘Koma ngati simukawapitikitsa anthu onsewo,+ ndithu amene mukasiyewo adzakhala ngati zitsotso m’maso mwanu, ndiponso ngati minga yokulasani m’nthiti mwanu. Ndithu adzakusautsani m’dziko limene mudzakhalamo.+ Oweruza 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Poyankha iwo anati: “Nyamukani, tiyeni tipite kukamenyana nawo, chifukwa ife taliona dzikolo ndipo ndi labwino kwambiri.+ Mukuzengerezatu. Musachite ulesi, koma nyamukani mukatenge dzikolo kukhala lanu.+ Miyambo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+
55 “‘Koma ngati simukawapitikitsa anthu onsewo,+ ndithu amene mukasiyewo adzakhala ngati zitsotso m’maso mwanu, ndiponso ngati minga yokulasani m’nthiti mwanu. Ndithu adzakusautsani m’dziko limene mudzakhalamo.+
9 Poyankha iwo anati: “Nyamukani, tiyeni tipite kukamenyana nawo, chifukwa ife taliona dzikolo ndipo ndi labwino kwambiri.+ Mukuzengerezatu. Musachite ulesi, koma nyamukani mukatenge dzikolo kukhala lanu.+
4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+