Ekisodo 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzawathamangitsa pamaso pako pang’onopang’ono kufikira mutaberekana ndi kulanda dzikolo.+ Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+ Yoswa 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yoswa anafunsa ana a Isiraeli kuti: “Kodi muzengereza mpaka liti osapita kukalanda dziko+ limene Yehova Mulungu wa makolo anu wakupatsani?+
30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+
3 Choncho Yoswa anafunsa ana a Isiraeli kuti: “Kodi muzengereza mpaka liti osapita kukalanda dziko+ limene Yehova Mulungu wa makolo anu wakupatsani?+