Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 16:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Sarai mkazi wa Abulamu anapereka Hagara, kapolo wake Mwiguputo, kwa mwamuna wake Abulamu kuti akhale mkazi wake.+ Zimenezi zinachitika Abulamu atakhala zaka 10 m’dziko la Kanani.

  • Ekisodo 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ngati mbuye wake sanakondwere naye kuti akhale mkazi wake wamng’ono+ koma wamulola kuwomboledwa, mbuyeyo alibe ufulu womugulitsa kwa anthu a mtundu wina chifukwa wam’chitira zachinyengo.

  • 2 Samueli 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.

  • 2 Mbiri 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Rehobowamu anali kukonda kwambiri Maaka mdzukulu wa Abisalomu kuposa akazi ake ena onse+ ndi adzakazi* ake, pakuti iye anakwatira akazi 18, ndiponso anali ndi adzakazi 60. Iye anabereka ana aamuna 28 ndi ana aakazi 60.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena