Oweruza 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano masiku amenewo, mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndiyeno Mlevi wina anakhala kwa kanthawi m’dera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu.+ Patapita nthawi, anatenga mkazi wa ku Betelehemu,+ ku Yuda, kukhala mdzakazi wake.+
19 Tsopano masiku amenewo, mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndiyeno Mlevi wina anakhala kwa kanthawi m’dera lamapiri lakutali kwambiri la Efuraimu.+ Patapita nthawi, anatenga mkazi wa ku Betelehemu,+ ku Yuda, kukhala mdzakazi wake.+