Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amunawo anathamangira azondi aja, cha kowolokera mtsinje wa Yorodano.+ Ndipo atangotuluka pachipata cha mzinda, nthawi yomweyo chipatacho chinatsekedwa.

  • Oweruza 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno amuna a ku Giliyadi anakatchinga powolokera Yorodano+ anthu a ku Efuraimu asanafike. Anthu othawa a ku Efuraimu akanena kuti: “Ndiloleni ndiwoloke,” pamenepo amuna a ku Giliyadi anali kumufunsa kuti: “Kodi ndiwe wa ku Efuraimu?” Akayankha kuti: “Ayi!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena