Oweruza 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo anawauza kuti: “Nditsatireni,+ chifukwa Yehova wapereka Amowabu, adani anu, m’manja mwanu.”+ Atatero, anam’tsatira kukatsekereza Amowabu pamalo owolokera mtsinje+ wa Yorodano, ndipo sanalole aliyense kuwoloka.
28 Pamenepo anawauza kuti: “Nditsatireni,+ chifukwa Yehova wapereka Amowabu, adani anu, m’manja mwanu.”+ Atatero, anam’tsatira kukatsekereza Amowabu pamalo owolokera mtsinje+ wa Yorodano, ndipo sanalole aliyense kuwoloka.