Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno mmodzi wa iwo anapitiriza kuti: “Ndidzabweranso kwa iwe ndithu chaka chamawa nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara mkazi wako adzakhala ndi mwana wamwamuna.”+ Pa nthawiyi n’kuti Sara akumvetsera, ali pakhomo la hemayo. Ndipo mlendoyo anali atafulatira hemayo.

  • 1 Samueli 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pamene chaka chinkatha, Hana anatenga pakati ndipo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lake+ Samueli,* chifukwa anati, “ndinam’pempha+ kwa Yehova.”

  • 2 Mafumu 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Elisa anati: “Chaka chamawa nthawi ngati yomwe ino mudzakhala mukuyangata mwana wamwamuna.”+ Koma mayiyo atamva anati: “Iyayi mbuyanga, munthu wa Mulungu woona! Musandinamize ine kapolo wanu.”

  • Luka 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya, chifukwa pembedzero lako lamveka ndithu.+ Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna, ndipo udzamutche Yohane.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena