Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+

  • Rute 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pamenepo Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa amoyo ndi akufa,+ am’dalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+

  • Salimo 31:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndikomereni mtima ine mtumiki wanu.+

      Ndipulumutseni mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+

  • Salimo 31:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova adalitsike,+

      Pakuti wandisonyeza modabwitsa kukoma mtima kosatha+ mumzinda wozingidwa ndi adani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena