Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+ Salimo 63:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti mwandithandiza,+Ndipo mumthunzi wa mapiko anu ndimafuula mosangalala.+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+ Salimo 63:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti mwandithandiza,+Ndipo mumthunzi wa mapiko anu ndimafuula mosangalala.+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+
4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.