Deuteronomo 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, atenge dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la m’bale wake lisafafanizike mu Isiraeli.+ Rute 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova akudalitseni.+ Aliyense apeze mpumulo+ m’nyumba ya mwamuna wake.” Kenako anawapsompsona.+ Pamenepo iwo anayamba kulira mokweza mawu,
6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, atenge dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la m’bale wake lisafafanizike mu Isiraeli.+
9 Yehova akudalitseni.+ Aliyense apeze mpumulo+ m’nyumba ya mwamuna wake.” Kenako anawapsompsona.+ Pamenepo iwo anayamba kulira mokweza mawu,