1 Samueli 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yonatani anauzanso Davide kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli+ akhale mboni,+ ndidzalankhula ndi bambo anga mawa kapena mkuja, ndipo ngati alibe chifukwa ndi iwe Davide, ndithu ine ndikutumizira uthenga wokudziwitsa zimenezi.
12 Yonatani anauzanso Davide kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli+ akhale mboni,+ ndidzalankhula ndi bambo anga mawa kapena mkuja, ndipo ngati alibe chifukwa ndi iwe Davide, ndithu ine ndikutumizira uthenga wokudziwitsa zimenezi.