1 Samueli 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Alonda a Sauli ku Gibeya+ wa ku Benjamini anaona zimene zinali kuchitika, ndipo anaona kuti chipwirikiti chafalikira paliponse mumsasamo.+
16 Alonda a Sauli ku Gibeya+ wa ku Benjamini anaona zimene zinali kuchitika, ndipo anaona kuti chipwirikiti chafalikira paliponse mumsasamo.+