Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Tsopano munthu+ akaona wina akuchita tchimo, kapena wamva kuti wina wachita tchimo,+ munthu ameneyo ndi mboni. Akamva chilengezo* kuti akachitire umboni za wochimwayo koma iye osapita kukanena,+ ndiye kuti wachimwa. Ayenera kuyankha mlandu wa cholakwa chakecho.

  • 1 Samueli 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Eli anali wokalamba kwambiri ndipo anamva+ zonse zimene ana ake anali kuchitira+ Aisiraeli onse, komanso anamva kuti anali kugona ndi akazi+ otumikira pakhomo la chihema chokumanako.+

  • Yohane 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndikanapanda kubwera kudzalankhula nawo, akanakhala opanda tchimo,+ koma tsopano alibe chodzilungamitsira pa tchimo lawo.+

  • Yakobo 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero, ngati munthu akudziwa kuchita chabwino koma sakuchichita,+ akuchimwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena