2 Samueli 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Davide anati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya kuti lero mukhale otsutsana+ nane? Kodi mu Isiraeli muyenera kuphedwa munthu aliyense lero?+ Kodi ine sindikudziwa bwino kuti lero ndine mfumu ya Isiraeli?” Miyambo 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi zimateteza mfumu,+ ndipo chifukwa cha kukoma mtima kosatha kumeneko mfumu imakhazikitsa mpando wake wachifumu.+ Aroma 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+
22 Koma Davide anati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya kuti lero mukhale otsutsana+ nane? Kodi mu Isiraeli muyenera kuphedwa munthu aliyense lero?+ Kodi ine sindikudziwa bwino kuti lero ndine mfumu ya Isiraeli?”
28 Kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi zimateteza mfumu,+ ndipo chifukwa cha kukoma mtima kosatha kumeneko mfumu imakhazikitsa mpando wake wachifumu.+
19 Okondedwa, musabwezere choipa,+ koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Pakuti Malemba amati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine, watero Yehova.”+