Miyambo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Monga chipale chofewa m’chilimwe ndiponso mvula pa nthawi yokolola,+ momwemonso ulemerero suyenerera munthu wopusa.+
26 Monga chipale chofewa m’chilimwe ndiponso mvula pa nthawi yokolola,+ momwemonso ulemerero suyenerera munthu wopusa.+