1 Samueli 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi ino si nyengo yokolola tirigu?+ Ndifuulira+ Yehova kuti abweretse mabingu ndi mvula.+ Pamenepo mudziwa ndi kuona kuti choipa chimene mwachita pamaso pa Yehova n’chachikulu,+ pakuti mwapempha kuti mukhale ndi mfumu.”
17 Kodi ino si nyengo yokolola tirigu?+ Ndifuulira+ Yehova kuti abweretse mabingu ndi mvula.+ Pamenepo mudziwa ndi kuona kuti choipa chimene mwachita pamaso pa Yehova n’chachikulu,+ pakuti mwapempha kuti mukhale ndi mfumu.”