Esitere 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake, Mfumu Ahasiwero analemekeza Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ ndipo anam’kweza+ ndi kum’patsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse amene mfumuyo inali nawo.+ Miyambo 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapolo akamalamulira monga mfumu,+ munthu wopusa akakhuta,+ Mlaliki 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndaonapo antchito atakwera pamahatchi,* koma akalonga akuyenda pansi ngati antchito.+
3 Pambuyo pake, Mfumu Ahasiwero analemekeza Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ ndipo anam’kweza+ ndi kum’patsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse amene mfumuyo inali nawo.+