1 Samueli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+ 2 Samueli 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka, pamenepo ukachitepo kanthu mwachangu,+ chifukwa pa nthawiyo Yehova adzakhala atatsogola kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”+ 2 Mafumu 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iye anati: “Usaope,+ popeza ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”+ Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+ Miyambo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pereka ntchito zako kwa Yehova,+ ndipo zolinga zako ndithu zidzakhazikika.+
6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+
24 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za baka, pamenepo ukachitepo kanthu mwachangu,+ chifukwa pa nthawiyo Yehova adzakhala atatsogola kukapha gulu lankhondo la Afilisiti.”+