Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano pita ukaphe Aamaleki+ ndi kuwawononga+ pamodzi ndi zonse zimene ali nazo. Usakawamvere chisoni, ukawaphe ndithu. Ukaphe+ mwamuna ndi mkazi, mwana wamng’ono ndi mwana woyamwa,+ ng’ombe ndi nkhosa, ngamila ndi bulu.’”+

  • Yobu 31:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+

      Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera?

  • Miyambo 10:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Njira ya Yehova ndiyo malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+ koma anthu ochita zopweteka ena adzawonongedwa.+

  • Miyambo 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsoka limatsatira ochimwa,+ koma olungama ndi amene amalandira mphoto zabwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena