Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+

      Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+

  • Salimo 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova ndiye thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso Wopereka chipulumutso kwa ine.+

      Mulungu wanga ndiye thanthwe langa. Ine ndidzathawira kwa iye.+

      Iye ndiye chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso ndiponso ndiye malo anga okwezeka achitetezo.+

  • Salimo 61:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti inu mwakhala pothawirapo panga,+

      Nsanja yolimba pamaso pa mdani.+

  • Miyambo 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena