Salimo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+ Salimo 124:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo madzi akanatikokolola,+Mtsinje wamphamvu ukanatimiza.+ Maliro 3:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Madzi asefukira ndi kumiza mutu wanga,+ moti ndanena kuti: “Ndifa basi!”+
6 Pa chifukwa chimenechi, aliyense wokhulupirika adzapemphera kwa inu,+Pa nthawi imene inu mungapezeke.+Ndipo madzi ambiri osefukira sadzamukhudza ngakhale pang’ono.+