Salimo 18:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mulungu woona ndiye Wobwezera adani anga.+Iye amagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika kunsi kwa mapazi anga.+ Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Salimo 144:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+ 1 Akorinto 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti ayenera kulamulira monga mfumu kufikira Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi+ ake.
47 Mulungu woona ndiye Wobwezera adani anga.+Iye amagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika kunsi kwa mapazi anga.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+