1 Mbiri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Ndipatse malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe, kuti mliriwu+ uthe pakati pa anthuwa. Ndikupatsa ndalama+ zake zonse.”+
22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Ndipatse malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe, kuti mliriwu+ uthe pakati pa anthuwa. Ndikupatsa ndalama+ zake zonse.”+