-
2 Samueli 3:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako Abineri anauza Davide kuti: “Ndiloleni ndinyamuke ndi kupita kuti ndikasonkhanitse Isiraeli yense kwa mbuyanga mfumu, kuti anthuwo achite pangano ndi inu ndipo mudzakhaladi mfumu pa zonse zimene moyo wanu umalakalaka.”+ Pamenepo Davide analola Abineri kupita ndipo ananyamukadi mwamtendere.+
-