Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kuwonjezera apo, inatumiza uthenga kwa Yehosafati mfumu ya Yuda, wakuti: “Mfumu ya Mowabu yandipandukira. Kodi upita nane kukamenya nkhondo ku Mowabu?” Yehosafati anayankha kuti: “Inde ndipita.+ Iwe ndi ine ndife amodzi. Anthu ako ndi anthu anga ndi amodzi.+ Mahatchi anga n’chimodzimodzi ndi mahatchi ako.”

  • 2 Mbiri 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ahabu mfumu ya Isiraeli anafunsa Yehosafati mfumu ya Yuda kuti: “Kodi upita nane ku Ramoti-giliyadi?”+ Yehosafati anamuyankha kuti: “Iwe ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu ako ndi amodzi, ndipo ali nawe limodzi pankhondoyi.”+

  • Miyambo 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+

  • 2 Akorinto 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena