1 Mafumu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako inafunsa Yehosafati kuti: “Kodi upita nane kunkhondo ku Ramoti-giliyadi?”+ Yehosafati anayankha mfumu ya Isiraeliyo kuti: “Iwe ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu ako ndi amodzi.+ Mahatchi anga n’chimodzimodzi ndi mahatchi ako.” 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+
4 Kenako inafunsa Yehosafati kuti: “Kodi upita nane kunkhondo ku Ramoti-giliyadi?”+ Yehosafati anayankha mfumu ya Isiraeliyo kuti: “Iwe ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu ako ndi amodzi.+ Mahatchi anga n’chimodzimodzi ndi mahatchi ako.”
14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+