2 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo. Yeremiya 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo akuuza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ ndipo akuuza mwala kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Iwo andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti, ‘Chonde, bwerani mudzatipulumutse!’+ Yeremiya 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kum’mawa imamwazira fumbi.+ Sindidzawaonetsa nkhope yanga,+ koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”
6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo.
27 Iwo akuuza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ ndipo akuuza mwala kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Iwo andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti, ‘Chonde, bwerani mudzatipulumutse!’+
17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kum’mawa imamwazira fumbi.+ Sindidzawaonetsa nkhope yanga,+ koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”