2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+ 1 Yohane 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,+ koma muziyesa mawu ouziridwawo kuti muone ngati ali ochokeradi kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri onyenga ambiri alowa m’dziko.+
4 Okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,+ koma muziyesa mawu ouziridwawo kuti muone ngati ali ochokeradi kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri onyenga ambiri alowa m’dziko.+