2 Mbiri 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Zedekiya+ mwana wa Kenaana+ anayandikira Mikaya+ ndipo anam’menya mbama.+ Kenako anati: “Kodi mzimu wa Yehova wachoka bwanji kwa ine n’kukalankhula ndi iwe?”+
23 Tsopano Zedekiya+ mwana wa Kenaana+ anayandikira Mikaya+ ndipo anam’menya mbama.+ Kenako anati: “Kodi mzimu wa Yehova wachoka bwanji kwa ine n’kukalankhula ndi iwe?”+