Genesis 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iyeyo anapita patsogolo pawo, n’kuyamba kugwada, n’kumaweramitsa nkhope yake pansi mpaka nthawi 7. Anachita zimenezi mpaka kufika pafupi ndi m’bale wakeyo.+ Genesis 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, Yosefe anachotsa anawo pambali pa mawondo a bambo ake. Kenako, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ Ekisodo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi yomweyo Mose anatuluka kukachingamira apongozi ake, ndipo anagwada n’kuwaweramira, kenako n’kuwapsompsona.+ Pamenepo anayamba kulonjerana ndi kufunsana za moyo. Kenako anapita kukalowa m’hema.
3 Koma iyeyo anapita patsogolo pawo, n’kuyamba kugwada, n’kumaweramitsa nkhope yake pansi mpaka nthawi 7. Anachita zimenezi mpaka kufika pafupi ndi m’bale wakeyo.+
12 Atatero, Yosefe anachotsa anawo pambali pa mawondo a bambo ake. Kenako, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
7 Nthawi yomweyo Mose anatuluka kukachingamira apongozi ake, ndipo anagwada n’kuwaweramira, kenako n’kuwapsompsona.+ Pamenepo anayamba kulonjerana ndi kufunsana za moyo. Kenako anapita kukalowa m’hema.