Ekisodo 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nsalu yotchingayi uipachike m’munsi mwa ngowe zolumikizira nsalu zapamwamba pa chihema, ndipo uike likasa la umboni+ kuseri kwa nsalu yotchingayi. Nsaluyi ikhale malire pakati pa Malo Oyera+ ndi Malo Oyera Koposa.+ Ekisodo 40:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo analowetsa Likasa m’chihema chopatulika ndi kuika nsalu yotchinga+ pamalo ake, kutchinga likasa la umboni,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
33 Nsalu yotchingayi uipachike m’munsi mwa ngowe zolumikizira nsalu zapamwamba pa chihema, ndipo uike likasa la umboni+ kuseri kwa nsalu yotchingayi. Nsaluyi ikhale malire pakati pa Malo Oyera+ ndi Malo Oyera Koposa.+
21 Pamenepo analowetsa Likasa m’chihema chopatulika ndi kuika nsalu yotchinga+ pamalo ake, kutchinga likasa la umboni,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.