1 Mafumu 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ansembe anabweretsa likasa+ la pangano la Yehova kumalo ake,+ kuchipinda chamkati cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+ Aheberi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe,+ ndi likasa la pangano.+ Likasa lonseli linali lokutidwa ndi golide.+ M’likasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana.+ Munalinso ndodo ya Aroni imene inaphuka ija,+ komanso miyala yosema+ ya pangano.
6 Kenako ansembe anabweretsa likasa+ la pangano la Yehova kumalo ake,+ kuchipinda chamkati cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+
4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe,+ ndi likasa la pangano.+ Likasa lonseli linali lokutidwa ndi golide.+ M’likasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana.+ Munalinso ndodo ya Aroni imene inaphuka ija,+ komanso miyala yosema+ ya pangano.