2 Mbiri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Koma kodi Mulungu angakhaledi ndi anthu padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+ Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+
18 “Koma kodi Mulungu angakhaledi ndi anthu padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+