29 ndiyeno anthuwo akapereka pemphero lililonse,+ pempho lililonse lopempha chifundo+ limene munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli+ angapemphe, chifukwa aliyense wa iwo akudziwa mliri wake+ ndi ululu wake, ndipo aliyense akatambasula manja ake kuwalozetsa kunyumba ino,+