38 ndiyeno anthuwo akapereka pemphero lililonse,+ pempho lililonse lopempha chifundo+ limene munthu aliyense kapena anthu anu onse Aisiraeli angapemphe,+ chifukwa aliyense wa iwo akudziwa ululu wa mumtima mwake,+ ndipo iwo akatambasula manja awo kuwalozetsa kunyumba ino,+