-
Danieli 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma Danieli atangodziwa kuti lamulo limeneli lasainidwa, analowa m’nyumba mwake, ndipo mawindo a nyumba yake oyang’ana ku Yerusalemu+ anali otsegula. M’nyumbamo, iye anali kugwada ndi kupemphera+ kwa Mulungu wake ndi kumutamanda+ katatu pa tsiku,+ monga mmene anali kuchitira nthawi zonse lamuloli lisanasainidwe.+
-