Ekisodo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+ Deuteronomo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo+ ndipo Yehova Mulungu wako anakutulutsa kumeneko ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula.+ N’chifukwa chake Yehova Mulungu wako anakulamula kuti uzisunga tsiku la sabata.+ Yeremiya 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli m’dziko la Iguputo+ pogwiritsa ntchito zizindikiro, zozizwitsa,+ dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+
6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+
15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo+ ndipo Yehova Mulungu wako anakutulutsa kumeneko ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula.+ N’chifukwa chake Yehova Mulungu wako anakulamula kuti uzisunga tsiku la sabata.+
21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli m’dziko la Iguputo+ pogwiritsa ntchito zizindikiro, zozizwitsa,+ dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+