Salimo 92:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu oipa akamaphuka ngati msipu,+Ndipo anthu onse ochita zopweteka anzawo akamaphuka ngati maluwa,Amatero kuti awonongeke kwamuyaya.+ Yesaya 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+ Yakobo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzuwa limatuluka ndi kutentha kwake n’kufotetsa zomera, ndipo maluwa a zomerazo amathothoka. Kukongola kwake kumatha. Momwemonso munthu wachuma adzafa akutsatira njira ya moyo wake.+
7 Anthu oipa akamaphuka ngati msipu,+Ndipo anthu onse ochita zopweteka anzawo akamaphuka ngati maluwa,Amatero kuti awonongeke kwamuyaya.+
7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+
11 Dzuwa limatuluka ndi kutentha kwake n’kufotetsa zomera, ndipo maluwa a zomerazo amathothoka. Kukongola kwake kumatha. Momwemonso munthu wachuma adzafa akutsatira njira ya moyo wake.+