Yoswa 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale+ kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka. Yoswa 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano anatenga amuna pafupifupi 5,000, nawabisa+ pakati pa Beteli+ ndi Ai, kumadzulo kwa mzinda wa Ai. Oweruza 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Isiraeli anaika amuna kuti abisalire+ mzinda wonse wa Gibeya. Oweruza 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno amuna amene anabisala aja, mwamsanga anathamanga kukalowa m’Gibeya.+ Atalowa mumzindamo,+ anamwazikana ndi kukantha mzinda wonse ndi lupanga.+
4 Anawalamula kuti: “Inu mukabisale+ kumbuyo kwa mzindawo. Musakakhale patali kwambiri ndi mzindawo, ndipo nonsenu mukakhale okonzeka.
12 Tsopano anatenga amuna pafupifupi 5,000, nawabisa+ pakati pa Beteli+ ndi Ai, kumadzulo kwa mzinda wa Ai.
37 Ndiyeno amuna amene anabisala aja, mwamsanga anathamanga kukalowa m’Gibeya.+ Atalowa mumzindamo,+ anamwazikana ndi kukantha mzinda wonse ndi lupanga.+